1 Yohane 1:7 BL92

7 koma ngati tiyenda m'kuunika, mongalye ali m'kuunika, tiyanjana wina ndi mnzace, ndipo mwazi wa Yesu Mwana wace utisambitsa kuticotsera ucimo wonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 1

Onani 1 Yohane 1:7 nkhani