10 M'menemo aoneka ana a Mulungu, ndi ana a mdierekezi: yense wosacita cilungamo siali wocokera mwa Mulungu; ndi iye wosakonda mbale wace.
Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 3
Onani 1 Yohane 3:10 nkhani