24 Ndipo 6 munthu amene asunga malamulo ace akhala mwa iye, ndi iye mwa munthuyo. Ndipo 7 m'menemo tizindikira kuti akhala mwa ife, kucokera mwa Mzimu amene anatipatsa ife.
Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 3
Onani 1 Yohane 3:24 nkhani