10 Umo muli cikondi, sikuti ife tinakonda Mulungu, koma kuti iye anatikonda ife, ndipo anatuma Mwana wace akhale ciombolo cifukwa ca macime athu.
Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 4
Onani 1 Yohane 4:10 nkhani