20 Munthu akati, kuti, Ndikonda Mulungu, nadana naye mbale wace, ali wabodza: pakuti iye wosakonda mbale ware amene wamuona, sakhoza kukonda Mulungu amene sanamuona.
Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 4
Onani 1 Yohane 4:20 nkhani