2 Petro 3:12 BL92

12 akuyembekezera ndi kufulumira kwa kudza kwace kwa tsiku la Mulungu, m'menemo miyamba potentha mota idzakanganuka, ndi zam'mwamba zidzasungunuka ndi kutentha kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 3

Onani 2 Petro 3:12 nkhani