2 Timoteo 2:14 BL92

14 Uwakumbutse izi, ndi kuwacitira umboni pamaso pa Ambuye, kuti asacite makani ndi mau osapindulitsa kanthu, koma ogwetsa iwo akumva.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 2

Onani 2 Timoteo 2:14 nkhani