2 Timoteo 2:15 BL92

15 Ucite cangu kudzionetsera kwa Mulungu wobvomerezeka, wanchito wopanda cifukwa ca kucita manyazi, wolunjika nao bwino mau a coonadi.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 2

Onani 2 Timoteo 2:15 nkhani