6 Koma apemphe ndi cikhulupiriro, wosakayika konse; pakuti wokayikayo afanana ndi pfunde la nyanja lotengeka ndi mphepo ndi kuwinduka nayo.
Werengani mutu wathunthu Yakobo 1
Onani Yakobo 1:6 nkhani