Maliro 1:16 BL92

16 Cifukwa ca zimenezi ndilira; diso langa, diso langatu likudza madzi:Pakuti wonditonthoza, wotsitsimutsa moyo wanga, anditarikira;Ana anga asungulumwa, pakuti adaniwo apambana.

Werengani mutu wathunthu Maliro 1

Onani Maliro 1:16 nkhani