20 Onani Yehova, nimupenye, mwacitira ayani ici?Kodi akazi adzadya zipatso zao, kunena ana amene anawaseweza?Kodi wansembe ndi mneneri adzaphedwa m'malo opatulika a Ambuye?
Werengani mutu wathunthu Maliro 2
Onani Maliro 2:20 nkhani