21 Wamng'ono ndi nkhalamba agona pansi m'makwalala;Anamwali ndi anyamata anga agwa ndi lupanga;Munawapha tsiku la mkwiyo wanu, munawagwaza osacitira cisoni.
Werengani mutu wathunthu Maliro 2
Onani Maliro 2:21 nkhani