Maliro 2:5 BL92

5 Yehova wasanduka mdani, wameza Israyeli;Wameza zinyumba zace zonse, wapasula malinga ace;Nacurukitsira mwana wamkazi wa Yuda maliro ndi cibumo.

Werengani mutu wathunthu Maliro 2

Onani Maliro 2:5 nkhani