Maliro 4:3 BL92

3 Angakhale ankhandwe amapatsa bere, nayamwitsa ana ao;Koma mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga wasanduka wankhanza, ngati nthiwatiwa za m'cipululu.

Werengani mutu wathunthu Maliro 4

Onani Maliro 4:3 nkhani