1 Petro 4:6 BL92

6 Pakuti cifukwa ca ici walalikidwa Uthenga Wabwino kwa iwonso adafawo, kuti akaweruzidwe monga mwa anthu m'thupi, koma akakhale ndi moyo monga mwa Mulungu mumzimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 4

Onani 1 Petro 4:6 nkhani