1 Timoteo 1:13 BL92

13 ndingakhale kale ndinali wamwano, ndi wolondalonda, ndi wacipongwe; komatu anandicitira cifundo, popeza ndinazicita wosazindikira, wosakhulupirira;

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 1

Onani 1 Timoteo 1:13 nkhani