10 Pakuti kukalingako tlgwiritsa nchito ndi kuyesetsa, cifukwa ciyembekezo cathu tiri naco pa Mulungu wamoyo, amene ali Mpulumutsi wa anthu onse, makamaka wa okhulupira.
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 4
Onani 1 Timoteo 4:10 nkhani