6 Ngati ukumbutsa abale zinthu izi, udzakhala mtumiki wabwino wa Kristu Yesu, woleredwa m'mauwo a cikhulupiriro, ndi malangizo abwino amene udawatsata;
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 4
Onani 1 Timoteo 4:6 nkhani