1 Timoteo 5:4 BL92

4 Koma ngati wamasiye wina ali nao ana kapena adzukulu, ayambe aphunzire iwo kucitira ulemu a m'banja lao, ndi kubwezera akuwabala; pakuti ici ncolandirika pamaso pa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 5

Onani 1 Timoteo 5:4 nkhani