9 Koma iwo akufuna kukhala acuma amagwa m'ciyesero ndi m'msampha, ndi m'zilakolako zambiri zopusa ndi zopweteka, zotere zonga zimiza anthu m'cionongekondi citayiko.
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 6
Onani 1 Timoteo 6:9 nkhani