Aefeso 1:7 BL92

7 Tiri ndi maomboledwe mwa mwazi wace, cikhululukiro ca zocimwa, monga mwa kulemera kwa cisomo cace,

Werengani mutu wathunthu Aefeso 1

Onani Aefeso 1:7 nkhani