3 amene ife tonsenso tinagonera pakati pao kale, m'zilakolako za thupi lathu, ndi kucita zifuniro za thupi, ndi za maganizo, ndipo tinali ana a mkwiyo cibadwire, monganso otsalawo;
Werengani mutu wathunthu Aefeso 2
Onani Aefeso 2:3 nkhani