Aefeso 5:33 BL92

33 Komanso inu, yense pa yekha, yense akonde mkazi wace wa iye yekha, monga adzikonda yekha; ndipo 2 mkaziyo akumbukile kuti aziopa mwamuna.

Werengani mutu wathunthu Aefeso 5

Onani Aefeso 5:33 nkhani