12 Onseamene afuna kuonekera okoma m'thupi, iwowa akukangamizani inu mudulidwe; cokhaco, cakuti angazunzike cifukwa ca mtanda wa Kristu.
Werengani mutu wathunthu Agalatiya 6
Onani Agalatiya 6:12 nkhani