15 Pakuti mdulidwe ulibe kanthu, kusadulidwakulibe kanthunso, komatu wolengedwa watsopano.
16 Ndipo onse amene atsatsa cilangizo ici, mtendere ndi cifundo zikhale pa iwo, ndi pa Israyeli wa Mulungu.
17 Kuyambira tsopano palibe munthu andibvute, pakuti ndiri nayo ine m'thupi mwanga mikwingwirima ya Yesu.
18 Cisomo ca Ambuye wathu Yesu Kristu cikhale ndi mzimu wanu, abale. Amen.