Nyimbo 3:10 BL92

10 Anapanga timilongoti tace ndi siliva,Ca pansi pace ndi golidi, mpando wace ndi nsaru yakuda,Pakati pace panayalidwa za cikondi ca ana akazi a ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 3

Onani Nyimbo 3:10 nkhani