Nyimbo 4:2 BL92

2 Mano ako akunga gulu la nkhosa zosengasenga,Zokwera kucokera kosamba;Yonse iri ndi ana awiri,Palibe imodzi yopoloza.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 4

Onani Nyimbo 4:2 nkhani