Nyimbo 5:13 BL92

13 Masaya ace akunga citipula cabzyalamo ndiwo,Ngati mitumbira yoyangapo masamba onunkhira:Milomo yace ikunga akakombo, pakukhapo madzi a nipa.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 5

Onani Nyimbo 5:13 nkhani