Nyimbo 6:11 BL92

11 Ndinatsikira ku munda wa ntedza,Kukapenya msipu wa m'cigwa,Kukapenya ngati pamipesa paphuka,Ngati pamakangaza patuwa maluwa.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 6

Onani Nyimbo 6:11 nkhani