7 umene anandiika ine mlaliki wace ndi mtumwi (ndinena zoona, wosanama ine), mphunzitsi wa amitundu m'cikhulupiriro ndi coonadi.
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 2
Onani 1 Timoteo 2:7 nkhani