1 Timoteo 2:8 BL92

8 Cifukwa cace ndifuna kuti amunawo apemphere pamalo ponse, ndi kukweza manja oyera, opanda mkwiyo ndi makani.

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 2

Onani 1 Timoteo 2:8 nkhani