9 Momwemonso, akazi adzibveke okha ndi cobvala coyenera, ndi manyazi, ndi cidziletso; osati ndi tsitsi lace loluka, ndi golidi kapena ngale, kapena maraya a mtengo wace wapatali;
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 2
Onani 1 Timoteo 2:9 nkhani