1 Timoteo 3:7 BL92

7 Kuyeneranso kuti iwo akunja adzakhoza kumcitira umboni wabwino; kuti ungamgwere mtonzo, ndi msampha wa mdierekezi.

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 3

Onani 1 Timoteo 3:7 nkhani