1 Timoteo 5:23 BL92

23 Usakhalenso wakumwa madzi okha, komatu ucite naye vinyo pang'ono, cifukwa ca mimba yako ndi zofoka zako zobwera kawiri kawiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 5

Onani 1 Timoteo 5:23 nkhani