17 Lamulira iwo acuma m'nthawi yino ya pansi pano, kuti asadzikuze, kapena asayembekezere cuma cosadziwika kukhala kwace, koma Mulungu, amene atipatsa ife zonse kocurukira, kuti tikondwere nazo;
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 6
Onani 1 Timoteo 6:17 nkhani