18 kuti acite zabwino, naeuruke ndi nchito zabwino, nakondwere kugawira ena, nayanjane;
19 nadzikundikire okha maziko okoma ku nyengo ikudzayi, kuti akagwire moyo weni weniwo.
20 Timoteo iwe, dikira cokusungitsa, ndi kulewa zokamba zopanda pace ndi zotsutsana za ici cichedwa cizindikiritso konama;
21 cimene ena pocibvomereza 1 adalakwa ndi kutaya cikhulupiriro. Cisomo cikhale nanu.