Aefeso 5:8 BL92

8 pakuti kale munali mdima, koma tsopano muli kuunika mwa Ambuye; yendani monga ana a kuunika,

Werengani mutu wathunthu Aefeso 5

Onani Aefeso 5:8 nkhani