Agalatiya 3:16 BL92

16 Ndipo malonjezano ananenedwa kwa Abrahamu ndi kwa mbeu yace, Sanena, Ndipo kwa zimbeu, ngati kunena zambiri; komatu ngati kunena imodzi, Ndipo kwa mbeu yako, ndiye Kristu.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 3

Onani Agalatiya 3:16 nkhani