13 Pakuti adakuitanani inu, abale, mukhale mfulu; cokhaco musacite nao ufulu wanu cothandizira thupi, komatu mwa cikondi citiranani ukapolo.
Werengani mutu wathunthu Agalatiya 5
Onani Agalatiya 5:13 nkhani