19 Ndipo anaimika dzanja lao kuti adzacotsa akazi ao; ndipo popeza adaparamuladi, anapereka nsembe nkhosa yamphongo ya zoweta pa kuparamula kwao.
Werengani mutu wathunthu Ezara 10
Onani Ezara 10:19 nkhani