Ezara 2:62 BL92

62 Awa anafunafuna maina ao m'buku la iwo owerengedwa mwa cibadwidwe cao, koma osawapeza; potero anacotsedwa ku nchito ya nsembe monga odetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Ezara 2

Onani Ezara 2:62 nkhani