13 Ndilamulira kuti onse a ana a Israyeli, ndi ansembe ao, ndi Alevi, m'ufumu wanga, ofuna eni ace kumuka ku Yerusalemu, apite nawe.
Werengani mutu wathunthu Ezara 7
Onani Ezara 7:13 nkhani