9 Sindidzacita mkwiyo wanga waukali, sindidzabwerera kuononga Efraimu; pakuti Ine ndine Mulungu, si munthu ai; Woyera wa pakati pako; ndipo sindidzalowa m'mudzi.
Werengani mutu wathunthu Hoseya 11
Onani Hoseya 11:9 nkhani