8 Ndidzakomana nao ngati cimbalangondo cocilanda ana ace, ndi kung'amba cokuta mtima wao; ndi pomwepo ndidzawalusira ngati mkango; cirombo cidzawamwetula.
Werengani mutu wathunthu Hoseya 13
Onani Hoseya 13:8 nkhani