Hoseya 2:11 BL92

11 Ndidzaleketsanso kusekerera kwace konse, madyerero ace, pokhala mwezi pace, ndi masabata ace, ndi masonkhano ace onse oikika.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 2

Onani Hoseya 2:11 nkhani