3 Tidziwe tsono, tilondole kudziwa Yehova; kuturuka kwace kwakonzekeratu ngati matanda kuca; ndipo adzatidzera ngati mvula, ngati mvula ya masika yakuthirira dziko.
Werengani mutu wathunthu Hoseya 6
Onani Hoseya 6:3 nkhani