10 Ndipo kudzikuza kwa Israyeli kumcitira umboni pamaso pace; koma sanabwerera kumka kwa Yehova Mulungu wao, kapena kumfunafuna mwa ici conse.
Werengani mutu wathunthu Hoseya 7
Onani Hoseya 7:10 nkhani