14 Nkhunda yangawe, yokhala m'ming'alu ya thanthwe, mobisika motsetsereka,Ndipenye nkhope yako, ndimve manako;Pakuti mau ako ngokoma, nkhope yako ndi kukongola.
Werengani mutu wathunthu Nyimbo 2
Onani Nyimbo 2:14 nkhani