3 Ngati maula pakati pa mitengo ya m'nkhalango,Momwemo wokondedwa wanga pakati pa ana amuna.Ndinakondwa pakukhala pa mthunzi wace,Zipatso zace zinatsekemera m'kamwa mwanga.
Werengani mutu wathunthu Nyimbo 2
Onani Nyimbo 2:3 nkhani