9 Wokondedwa wanga akunga mphoyo, pena mwana wa mbawala:Taona, aima patseri pa khoma pathu,Apenyera pazenera, Nasuzumira pamade.
Werengani mutu wathunthu Nyimbo 2
Onani Nyimbo 2:9 nkhani